Yoweli 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzagulitsa ana anu aamuna ndi aakazi kwa anthu a ku Yuda.+Iwo adzawagulitsa kwa anthu a ku Sheba, mtundu wa anthu akutali.Ine Yehova ndanena zimenezi.
8 Ndidzagulitsa ana anu aamuna ndi aakazi kwa anthu a ku Yuda.+Iwo adzawagulitsa kwa anthu a ku Sheba, mtundu wa anthu akutali.Ine Yehova ndanena zimenezi.