Yoweli 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova adzabangula kuchokera ku Ziyoni,Ndipo adzalankhula mokweza ali ku Yerusalemu. Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka.Koma Yehova adzakhala malo othawirako a anthu ake,+Malo achitetezo champhamvu kwa Aisiraeli. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Utumiki wa Ufumu,7/2013, tsa. 1 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 108, 156 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 255/1/1992, tsa. 105/15/1987, ptsa. 18-19
16 Yehova adzabangula kuchokera ku Ziyoni,Ndipo adzalankhula mokweza ali ku Yerusalemu. Kumwamba ndi dziko lapansi zidzagwedezeka.Koma Yehova adzakhala malo othawirako a anthu ake,+Malo achitetezo champhamvu kwa Aisiraeli.
3:16 Utumiki wa Ufumu,7/2013, tsa. 1 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 108, 156 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 255/1/1992, tsa. 105/15/1987, ptsa. 18-19