Yoweli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo opatulika,+Ndipo anthu achilendo* sadzadutsanso mmenemo.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:17 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 25
17 Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo opatulika,+Ndipo anthu achilendo* sadzadutsanso mmenemo.+