Yoweli 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:18 Nsanja ya Olonda,3/1/1999, tsa. 195/1/1998, tsa. 25
18 Nthawi imeneyo mʼmapiri akuluakulu mudzatuluka vinyo wotsekemera.+Mʼmapiri angʼonoangʼono mudzayenda mkaka.Ndipo mʼmitsinje yonse ya Yuda mudzayenda madzi. Kasupe adzatuluka mʼnyumba ya Yehova,+Ndipo adzathirira chigwa cha Mitengo ya Mthethe.