Yoweli 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+
19 Koma Iguputo adzasanduka bwinja,+Ndipo Edomu adzakhala chipululu chopanda kanthu.+Chifukwa cha nkhanza zimene anachitira anthu a ku Yuda,+Ndiponso chifukwa chokhetsa magazi a anthu osalakwa mʼdziko la Yudalo.+