Amosi 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 16
3 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Damasiko anandigalukira mobwerezabwereza,* sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapuntha Giliyadi ndi zida zopunthira zachitsulo.+