Amosi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzathyola mipiringidzo ya mageti a Damasiko.+Ndidzapha anthu a ku Bikati-aveni,Komanso wolamulira* ku Beti-edeni.Ndipo anthu a ku Siriya adzapita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, tsa. 22
5 Ndidzathyola mipiringidzo ya mageti a Damasiko.+Ndidzapha anthu a ku Bikati-aveni,Komanso wolamulira* ku Beti-edeni.Ndipo anthu a ku Siriya adzapita ku ukapolo ku Kiri,”+ watero Yehova.’