Amosi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzatumiza moto pampanda wa Gaza,+Ndipo udzawotcheratu nsanja zake zolimba.