Amosi 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wanena kuti,‘Popeza Turo anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo,Ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pachibale.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Tsiku la Yehova, tsa. 111
9 Yehova wanena kuti,‘Popeza Turo anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo,Ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pachibale.+