Amosi 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzayatsa mpanda wa Raba,+Ndipo motowo udzawotcheratu nsanja zake zolimba.Padzakhala mfuu ya nkhondo pa tsiku la nkhondo.Komanso mphepo yamkuntho pa tsiku la chimvula champhamvu.
14 Ndidzayatsa mpanda wa Raba,+Ndipo motowo udzawotcheratu nsanja zake zolimba.Padzakhala mfuu ya nkhondo pa tsiku la nkhondo.Komanso mphepo yamkuntho pa tsiku la chimvula champhamvu.