Amosi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Mowabu anandigalukira mobwerezabwereza,*+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.
2 “Yehova wanena kuti,‘“Popeza Mowabu anandigalukira mobwerezabwereza,*+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.