Amosi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Koma ine ndi amene ndinapha Aamori iwo akuona.+Aamoriwo anali aatali ngati mitengo ya mkungudza komanso amphamvu ngati mitengo ikuluikulu.Ndinawononga zipatso zawo mʼmwamba ndiponso mizu yawo pansi.+
9 ‘Koma ine ndi amene ndinapha Aamori iwo akuona.+Aamoriwo anali aatali ngati mitengo ya mkungudza komanso amphamvu ngati mitengo ikuluikulu.Ndinawononga zipatso zawo mʼmwamba ndiponso mizu yawo pansi.+