12 Yehova wanena kuti,
‘Ngati mmene mʼbusa amapulumutsira miyendo iwiri ya chiweto kapena kachidutswa ka khutu mʼkamwa mwa mkango,
Ndi mmenenso adzapulumukire Aisiraeli,
Amene akukhala pamipando yapamwamba ndiponso kugona pamabedi okongola ku Samariya.’+