Amosi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Aisiraeli chifukwa chondigalukira,+Ndidzalanganso maguwa ansembe a ku Beteli.+Nyanga za guwa lansembe zidzadulidwa nʼkugwa pansi.+
14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Aisiraeli chifukwa chondigalukira,+Ndidzalanganso maguwa ansembe a ku Beteli.+Nyanga za guwa lansembe zidzadulidwa nʼkugwa pansi.+