Amosi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Tamverani mawu awa, inu ngʼombe zazikazi za ku Basana,Amene mumakhala mʼphiri la Samariya,+Inu akazi amene mukuchitira zachinyengo anthu ovutika+ komanso kuphwanya anthu osauka.Ndipo mumauza amuna* anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 144/1/1989, tsa. 22
4 “Tamverani mawu awa, inu ngʼombe zazikazi za ku Basana,Amene mumakhala mʼphiri la Samariya,+Inu akazi amene mukuchitira zachinyengo anthu ovutika+ komanso kuphwanya anthu osauka.Ndipo mumauza amuna* anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’