-
Amosi 4:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walumbira mogwirizana ndi kuyera kwake kuti,
‘“Taonani! Masiku adzafika pamene iye adzakukolani ndi ngowe zokolera nyama nʼkukunyamulani.
Ndipo otsala adzawakola ndi mbedza.
-