Amosi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+
4 ‘Bwerani ku Beteli anthu inu kuti mudzachite zolakwa,*+Bwerani ku Giligala kuti mudzawonjezere machimo.+ Bweretsani nsembe zanu+ mʼmawa.Ndipo pa tsiku lachitatu, mubweretse chakhumi* chanu.+