Amosi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+Ndinagwetsa mvula mumzinda wina koma mumzinda wina sindinagwetse. Mvula inagwa mʼmunda umodziKoma mʼmunda wina, mmene simunagwe mvula, munauma.
7 ‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+Ndinagwetsa mvula mumzinda wina koma mumzinda wina sindinagwetse. Mvula inagwa mʼmunda umodziKoma mʼmunda wina, mmene simunagwe mvula, munauma.