Amosi 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Ndinakutumizirani mliri ngati wa ku Iguputo.+ Ndinapha anyamata anu ndi lupanga+ ndipo mahatchi anu analandidwa.+ Ndinachititsa kuti fungo lonunkha lamʼmisasa yanu lifike mʼmphuno mwanu,+Koma inu simunabwerere kwa ine,’ watero Yehova.
10 ‘Ndinakutumizirani mliri ngati wa ku Iguputo.+ Ndinapha anyamata anu ndi lupanga+ ndipo mahatchi anu analandidwa.+ Ndinachititsa kuti fungo lonunkha lamʼmisasa yanu lifike mʼmphuno mwanu,+Koma inu simunabwerere kwa ine,’ watero Yehova.