13 Taona! Iye ndi amene anapanga mapiri+ ndipo analenganso mphepo,+
Amafotokozera munthu zimene akuganiza,
Amachititsa kuwala kwa mʼbandakucha kukhala mdima,+
Ndiponso amaponda malo okwezeka a dziko lapansi.”+
Dzina lake ndi Yehova Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba.