Amosi 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti, ‘Mzinda umene unkapita kunkhondo ndi anthu 1,000, udzatsala ndi anthu 100.Ndipo mzinda umene unkapita kunkhondo ndi anthu 100, udzatsala ndi anthu 10. Zimenezi ndi zimene zidzachitikire nyumba ya Isiraeli.’+
3 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa wanena kuti, ‘Mzinda umene unkapita kunkhondo ndi anthu 1,000, udzatsala ndi anthu 100.Ndipo mzinda umene unkapita kunkhondo ndi anthu 100, udzatsala ndi anthu 10. Zimenezi ndi zimene zidzachitikire nyumba ya Isiraeli.’+