Amosi 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova wauza anthu a mʼnyumba ya Isiraeli kuti: ‘Ndifufuzeni kuti mupitirize kukhala ndi moyo.+