Amosi 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anthu ozindikira adzakhala chete pa nthawi imeneyo,Chifukwa idzakhala nthawi yoopsa.+