Amosi 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Padzakhala kulira mokweza mʼminda yonse ya mpesa,+Chifukwa ine ndidzadutsa pakati panu,’ watero Yehova.
17 ‘Padzakhala kulira mokweza mʼminda yonse ya mpesa,+Chifukwa ine ndidzadutsa pakati panu,’ watero Yehova.