Amosi 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi chidzakuchitikireni nʼchiyani pa tsiku la Yehova?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima, osati kuwala.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:18 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 15 Tsiku la Yehova, ptsa. 38-40
18 ‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi chidzakuchitikireni nʼchiyani pa tsiku la Yehova?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima, osati kuwala.+