-
Amosi 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Zidzakhala ngati munthu amene akuthawa mkango wakumana ndi chimbalangondo,
Ndipo pamene akulowa mʼnyumba nʼkugwira khoma, njoka ikumuluma.
-