Amosi 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo sindigwirizana nazo,+Komanso sindisangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera. Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:21 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 21-22
21 Ine ndimadana ndi zikondwerero zanu ndipo sindigwirizana nazo,+Komanso sindisangalala ndi fungo la nsembe zanu zoperekedwa pamisonkhano yanu yapadera.