Amosi 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chilungamo chiyende ngati madzi.+Ndiponso ngati mtsinje wosaphwa nthawi zonse.