Amosi 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu amʼnyumba ya Isiraeli,Kodi pamene munali mʼchipululu muja kwa zaka 40, munandipatsa nsembe zanyama ndi zopereka zina?+
25 Inu amʼnyumba ya Isiraeli,Kodi pamene munali mʼchipululu muja kwa zaka 40, munandipatsa nsembe zanyama ndi zopereka zina?+