Amosi 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pitani mukaone ku Kaline. Mukakachoka kumeneko mukapite ku Hamati Wamkulu,+Kenako mukapite ku Gati wa Afilisiti. Kodi mizinda imeneyi imaposa maufumu anu awiriwa?*Kapena kodi malo awo ndi aakulu kuposa malo anu?
2 Pitani mukaone ku Kaline. Mukakachoka kumeneko mukapite ku Hamati Wamkulu,+Kenako mukapite ku Gati wa Afilisiti. Kodi mizinda imeneyi imaposa maufumu anu awiriwa?*Kapena kodi malo awo ndi aakulu kuposa malo anu?