Amosi 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumamwera vinyo mʼmakapu akuluakulu,+Ndipo mumadzola mafuta apamwamba kwambiri. Komanso simukukhudzidwa* ndi tsoka lomwe linagwera Yosefe.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 20-213/15/2003, ptsa. 16-17
6 Mumamwera vinyo mʼmakapu akuluakulu,+Ndipo mumadzola mafuta apamwamba kwambiri. Komanso simukukhudzidwa* ndi tsoka lomwe linagwera Yosefe.+