-
Amosi 6:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Wachibale* adzabwera kudzawatulutsa nʼkuyamba kuwawotcha mmodzimmodzi. Adzatulutsa mafupa awo mʼnyumbamo, ndiyeno adzafunsa aliyense amene ali mʼzipinda zamkati kuti, “Kodi muli anthu enanso mmenemo?” Ndipo adzayankha kuti, “Mulibe!” Kenako adzamuuza kuti, “Khala chete! Chifukwa ino si nthawi yotchula dzina la Yehova.”’
-