Amosi 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi mahatchi angathamange pathanthwe?Kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ngʼombe? Chifukwa mwasintha chilungamo kukhala chomera chapoizoni,Ndipo mwasandutsa chipatso cha chilungamo kukhala chinthu chowawa.+
12 Kodi mahatchi angathamange pathanthwe?Kapena kodi munthu angalime pathanthwe ndi ngʼombe? Chifukwa mwasintha chilungamo kukhala chomera chapoizoni,Ndipo mwasandutsa chipatso cha chilungamo kukhala chinthu chowawa.+