Amosi 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti ‘Inu amʼnyumba ya Isiraeli, ine ndikubweretserani mtundu wa anthu.+Ndipo udzakuponderezani kuyambira ku Lebo-hamati*+ mpaka kuchigwa* cha Araba.’”
14 Tsopano Yehova, Mulungu wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti ‘Inu amʼnyumba ya Isiraeli, ine ndikubweretserani mtundu wa anthu.+Ndipo udzakuponderezani kuyambira ku Lebo-hamati*+ mpaka kuchigwa* cha Araba.’”