-
Amosi 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsanso masomphenya awa: Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, analamula kuti dziko lilangidwe ndi moto. Motowo unaumitsa madzi akuya ndiponso unawononga kachigawo ka dziko.
-