-
Amosi 7:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anandionetsanso masomphenya awa: Yehova anaima pamwamba pa khoma limene linamangidwa pogwiritsa ntchito chingwe chowongolera, ndipo anali ndi chingwe chowongolera mʼmanja mwake.
-