Amosi 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malo okwezeka a Isaki+ adzawonongedwa, ndipo malo opatulika a Isiraeli adzasakazidwa.+ Ine ndidzabwera kudzawononga nyumba ya Yerobowamu ndi lupanga.”+
9 Malo okwezeka a Isaki+ adzawonongedwa, ndipo malo opatulika a Isiraeli adzasakazidwa.+ Ine ndidzabwera kudzawononga nyumba ya Yerobowamu ndi lupanga.”+