Amosi 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.” Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 13
13 Koma usapitirize kunenera ku Beteli kuno,+ chifukwa ndi malo opatulika a mfumu+ ndiponso nyumba ya ufumuwu.”