Amosi 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso zamʼchilimwe.” Kenako Yehova anandiuza kuti: “Mapeto a anthu anga Aisiraeli afika ndipo sindidzawakhululukiranso.+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 Nsanja ya Olonda,10/1/2007, tsa. 146/15/2007, tsa. 124/1/1989, tsa. 22
2 Ndiyeno anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani Amosi?” Ndinayankha kuti: “Ndikuona dengu la zipatso zamʼchilimwe.” Kenako Yehova anandiuza kuti: “Mapeto a anthu anga Aisiraeli afika ndipo sindidzawakhululukiranso.+