Amosi 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu amene mumanena kuti: ‘Kodi chikondwerero cha nthawi imene mwezi watsopano waoneka chitha liti+ kuti tiyambe kugulitsa mbewu zathu?Sabata+ litha liti kuti tiyambe kutsatsa mbewu zathu, Kuti tichepetse muyezo wa efa,*Tiwonjezere kulemera kwa sekeli,*Komanso kuti tibere anthu ndi masikelo athu achinyengo?+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 11
5 Inu amene mumanena kuti: ‘Kodi chikondwerero cha nthawi imene mwezi watsopano waoneka chitha liti+ kuti tiyambe kugulitsa mbewu zathu?Sabata+ litha liti kuti tiyambe kutsatsa mbewu zathu, Kuti tichepetse muyezo wa efa,*Tiwonjezere kulemera kwa sekeli,*Komanso kuti tibere anthu ndi masikelo athu achinyengo?+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 11