Amosi 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu amene amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya+ nʼkumati:“Pali mulungu wako, iwe Dani,”+ Ndiponso “pali njira ya ku Beere-seba.”+ Adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+
14 Anthu amene amalumbira pa milungu yonama ya ku Samariya+ nʼkumati:“Pali mulungu wako, iwe Dani,”+ Ndiponso “pali njira ya ku Beere-seba.”+ Adzagwa ndipo sadzadzukanso.’”+