Amosi 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova wanena kuti, ‘Taonani, ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndikuyangʼana ufumu wochimwawo,Ndipo ndidzaufafaniza padziko lapansi.+ Koma nyumba ya Yakobo sindidzaifafaniza yonse.’+ Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:8 Nsanja ya Olonda,4/1/1989, tsa. 23
8 Yehova wanena kuti, ‘Taonani, ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ndikuyangʼana ufumu wochimwawo,Ndipo ndidzaufafaniza padziko lapansi.+ Koma nyumba ya Yakobo sindidzaifafaniza yonse.’+