Amosi 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Taonani, ine ndikupereka lamuloNdipo ndidzagwedeza nyumba ya Isiraeli pakati pa mitundu yonse,+Ngati mmene munthu amachitira posefa,Ndipo mwala sudzadutsa nʼkugwera pansi.
9 ‘Taonani, ine ndikupereka lamuloNdipo ndidzagwedeza nyumba ya Isiraeli pakati pa mitundu yonse,+Ngati mmene munthu amachitira posefa,Ndipo mwala sudzadutsa nʼkugwera pansi.