Amosi 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga atenge zinthu zotsala za Edomu.+Ndiponso za mitundu yonse ya anthu imene inkaitanira pa dzina langa,’ watero Yehova, amene akuchita zimenezi. Amosi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:12 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 5
12 Ndidzachita zimenezi kuti anthu anga atenge zinthu zotsala za Edomu.+Ndiponso za mitundu yonse ya anthu imene inkaitanira pa dzina langa,’ watero Yehova, amene akuchita zimenezi.