Amosi 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+
14 Ndidzasonkhanitsa ndi kubwezeretsa anthu anga Aisiraeli amene anatengedwa kupita ku ukapolo.+Iwo adzamanga mizinda imene ili yabwinja nʼkumakhalamo.+Adzalima minda ya mpesa nʼkumwa vinyo wake.+Adzalimanso minda nʼkudya zipatso zake.’+