Obadiya 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndi masomphenya a Obadiya:* Zimene Yehova Ambuye Wamkulu Koposa akunena zokhudza Edomu+ ndi izi: “Ife tamva uthenga wochokera kwa Yehova,Ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu amitundu ina kukanena kuti: ‘Konzekani! Tiyeni tikamenyane naye.’”+
1 Awa ndi masomphenya a Obadiya:* Zimene Yehova Ambuye Wamkulu Koposa akunena zokhudza Edomu+ ndi izi: “Ife tamva uthenga wochokera kwa Yehova,Ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu amitundu ina kukanena kuti: ‘Konzekani! Tiyeni tikamenyane naye.’”+