Obadiya 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale utamakhala mʼmwamba* ngati chiwombankhanga,Kapena utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi,Ine ndidzakugwetsapo pamenepo,” akutero Yehova.
4 Ngakhale utamakhala mʼmwamba* ngati chiwombankhanga,Kapena utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi,Ine ndidzakugwetsapo pamenepo,” akutero Yehova.