Obadiya 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Akuba atabwera kwa iwe, kapena mbava zitabwera usiku,Kodi sangabe zokhazo zimene akufuna? (Koma ndiye udzawonongedwatu!)* Kapena okolola mphesa atabwera kwa iwe,Kodi sangasiyeko zina zoti munthu nʼkukunkha?+ Obadiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5 Nsanja ya Olonda,11/1/2007, tsa. 13
5 “Akuba atabwera kwa iwe, kapena mbava zitabwera usiku,Kodi sangabe zokhazo zimene akufuna? (Koma ndiye udzawonongedwatu!)* Kapena okolola mphesa atabwera kwa iwe,Kodi sangasiyeko zina zoti munthu nʼkukunkha?+