Obadiya 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?
8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?