Obadiya 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Temani,+ asilikali ako adzachita mantha,+Chifukwa aliyense mʼdera lamapiri la Esau adzaphedwa.+
9 Iwe Temani,+ asilikali ako adzachita mantha,+Chifukwa aliyense mʼdera lamapiri la Esau adzaphedwa.+